6 Kodi kumeneku si kusala kudya kumene ndinakusankha: kumasula nsinga za zoipa, ndi kumasula zomanga gori, ndi kuleka otsenderezedwa amuke mfulu, ndi kuti mutyole magori onse?
Werengani mutu wathunthu Yesaya 58
Onani Yesaya 58:6 nkhani