15 Inde coona cisoweka; iye amene asiya coipa, zifunkhidwa zace; ndipo Yehova anaona ici, ndipo cidamuipira kuti palibe ciweruzo.
Werengani mutu wathunthu Yesaya 59
Onani Yesaya 59:15 nkhani