Yesaya 59:20 BL92

20 Ndipo Mombolo adzafika ku Ziyoni, ndi kwa iwo amene atembenuka kusiya kulakwa mwa Yakobo, ati Yehova.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 59

Onani Yesaya 59:20 nkhani