Yesaya 6:3 BL92

3 Ndipo wina anapfuula kwa mnzace, nati, Woyera, Woyera, Woyera, Yehova wa makamu; dziko lonse lapansi ladzala ulemerero wace.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 6

Onani Yesaya 6:3 nkhani