11 Zipata zako zidzakhalabe zotseguka, sizidzatsekedwa usana pena usiku, kuti abwere naco kwa iwe cuma ca amitundu, ndi mafumu ao otsogozedwa nao pamodzi.
Werengani mutu wathunthu Yesaya 60
Onani Yesaya 60:11 nkhani