2 Pakuti taona, mdima udzaphimba dziko lapansi, ndi mdima wa bii mitundu ya anthu; koma Yehova adzakuturukira, ndi ulemerero wace udzaoneka pa iwe.
Werengani mutu wathunthu Yesaya 60
Onani Yesaya 60:2 nkhani