Yesaya 61:11 BL92

11 Pakuti monga dziko liphukitsa mphundu zace, ndi monga munda umeretsa zobzalamo, momwemo Ambuye Yehova adzaphukitsa cilungamo ndi matamando pamaso pa amitundu onse.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 61

Onani Yesaya 61:11 nkhani