Yesaya 61:2 BL92

2 ndikalalikire caka cokomera Yehova, ndi tsiku lakubwezera la Mulungu wathu; ndikatonthoze mtima wa onse amene akulira maliro;

Werengani mutu wathunthu Yesaya 61

Onani Yesaya 61:2 nkhani