Yesaya 62:2 BL92

2 Ndipo amitundu adzaona cilungamo cako, ndi mafumu onse ulemerero wako; ndipo udzachedwa dzina latsopano, limene m'kamwa mwa Yehova mudzachula.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 62

Onani Yesaya 62:2 nkhani