Yesaya 63:10 BL92

10 Koma iwo anapandukira ndi kumvetsa cisoni mzimu wace woyera, cifukwa cace Iye anasandulika mdani wao, nawathira nkhondo Iye yekha.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 63

Onani Yesaya 63:10 nkhani