17 Yehova bwanji mwatisoceretsa kusiya njira zanu, ndi kuumitsa mitima yathu tisakuopeni? Bwerani, cifukwa ca atumiki anu, mafuko a colowa canu.
Werengani mutu wathunthu Yesaya 63
Onani Yesaya 63:17 nkhani