Yesaya 64:2 BL92

2 monga pamene moto uyatsa zitsamba, ndi moto uwiritsa madzi; kudziwitsa kwa amaliwongo anu dzina lanu, kuti amitundu anthunthumire pamaso panu,

Werengani mutu wathunthu Yesaya 64

Onani Yesaya 64:2 nkhani