1 Iwo amene sanafunsa za Ine andifunafuna; ndi iwo amene sanandipwaira andipeza; ndinati, Taonani Ine, taonani Ine, kwa mtundu umene sunachula dzina langa.
Werengani mutu wathunthu Yesaya 65
Onani Yesaya 65:1 nkhani