Yesaya 65:18 BL92

18 Koma khalani inu okondwa ndi kusangalala ku nthawi zonse ndi ici ndicilenga; pakuti taonani, ndilenga Yerusalemu wosangalala, ndi anthu ace okondwa.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 65

Onani Yesaya 65:18 nkhani