Yesaya 65:24 BL92

24 Ndipo padzakhala kuti iwo asanaitane Ine, ndidzayankha; ndipo ali cilankhulire, Ine ndidzamva.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 65

Onani Yesaya 65:24 nkhani