Yesaya 7:19 BL92

19 Ndipo zidzafika nizitera zonse m'zigwa zabwinja, ndi m'maenje a matanthwe, ndi paminga ponse, ndi pamabusa ponse.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 7

Onani Yesaya 7:19 nkhani