19 Ndipo pamene iwo adzati kwa iwe, Funa kwa olaula, ndi obwebweta, amene alira pyepye, nang'ung'udza; kodi anthu sadzafuna kwa Mulungu wao? Cifukwa ca amoyo, kodi adzafuna kwa akufa?
Werengani mutu wathunthu Yesaya 8
Onani Yesaya 8:19 nkhani