Yesaya 9:18 BL92

18 Pakuti kucimwa kwayaka ngati moto kumariza lunguzi ndi minga, inde kuyaka m'nkhalango ya m'thengo, ndipo zifuka capamwamba, m'mitambo yautsi yocindikira.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 9

Onani Yesaya 9:18 nkhani