Yesaya 9:21 BL92

21 Manase adzadya Efraimu ndi Efraimu adzadya Manase, ndipo iwo pamodzi adzadyana ndi Yuda. Mwa izi zonse mkwiyo wace sunacoke, koma dzanja lace liri citambasulire.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 9

Onani Yesaya 9:21 nkhani