Yesaya 10:14 BL92

14 dzanja langa lapeza monga cisa, cuma ca mitundu ya anthu, ndipo monga munthu asonkhanitsa mazira osiyidwa, ine ndasonkhanitsa dziko lonse lapansi, ndipo panalibe cogwedeza phiko, kapena cotsegula pakamwa, kapena colira pyepye.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 10

Onani Yesaya 10:14 nkhani