Yesaya 10:16 BL92

16 Cifukwa cace Ambuye, Yehova wa makamu, adzarumiza kuonda mwa onenepa ace; ndipo pansi pa ulemerero wace padzayaka kutentha, konga ngati kutentha kwa moto.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 10

Onani Yesaya 10:16 nkhani