Yesaya 10:17 BL92

17 Ndipo kuwala kwa Israyeli kudzakhala moto, ndi Woyera wace adzakhala lawi; ndipo lidzatentha ndi kuthetsa minga yace ndi lunguzi wace tsiku limodzi.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 10

Onani Yesaya 10:17 nkhani