Yesaya 10:18 BL92

18 Ndipo adzanyeketsa ulemerero wa m'nkhalango yace, ndi wa m'munda wace wopatsa bwino, moyo ndi thupi; ndipo padzakhala monga ngati pokomoka wonyamula mbendera.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 10

Onani Yesaya 10:18 nkhani