Yesaya 10:27 BL92

27 Ndipo padzakhala tsiku lomwelo, kuti katundu wace adzacoka pa phewa lako, ndi gori lace pakhosi pako; ndipo gori lidzathedwa cifukwa ca kudzoza mafuta.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 10

Onani Yesaya 10:27 nkhani