3 Ndipo mudzacita ciani tsiku lakudza woyang'anira, ndi cipasuko cocokera kutari? mudzathawira kwa yani kufuna kuthangatidwa? mudzasiya kuti ulemerero wanu?
Werengani mutu wathunthu Yesaya 10
Onani Yesaya 10:3 nkhani