Yesaya 11:12 BL92

12 Ndipo Iye adzaimika mbendera ya amitundu, ndipo adzasonkhanitsa oingitsidwa a Israyeli, namema obalalika a Yuda, kucokera ku madera anai a dziko lapansi.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 11

Onani Yesaya 11:12 nkhani