Yesaya 11:13 BL92

13 Ndipo nsanje ya Efraimu idzacoka, ndi iwo amene abvuta Yuda adzadulidwa; Efraimu sacitira nsanje Yuda, ndi Yuda sacitira nsanje Efraimu.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 11

Onani Yesaya 11:13 nkhani