14 Ndipo adzagudukira mapewa a Afilisti kumadzulo; pamodzi adzafunkha ana a kum'mawa; adzatambasula dzanja lao pa Edomu ndi pa Moabu; ndipo ana a Amoni adzawamvera.
Werengani mutu wathunthu Yesaya 11
Onani Yesaya 11:14 nkhani