Yesaya 13:21 BL92

21 Koma zirombo za m'cipululu zidzagona pamenepo; nyumba zao zidzadzala ndi zakukuwa; ndipo nthiwatiwa zidzakhala pamenepo, ndipo atonde adzajidimuka pamenepo,

Werengani mutu wathunthu Yesaya 13

Onani Yesaya 13:21 nkhani