22 Ndipo mimbulu idzalira m'maboma ao, ndi ankhandwe m'manyumba ao abwino; ndi nthawi yace iyandikira, ndi masiku ace sadzacuruka.
Werengani mutu wathunthu Yesaya 13
Onani Yesaya 13:22 nkhani