Yesaya 14:16 BL92

16 Iwo amene akuona iwe adzayang'anitsitsa iwe, nadzalingalira za iwe, ndi kuti, Kodi uyu ndi munthu amene ananthunthumiritsa dziko lapansi, amene anagwedeza maufumu;

Werengani mutu wathunthu Yesaya 14

Onani Yesaya 14:16 nkhani