Yesaya 19:15 BL92

15 Aigupto sadzakhala ndi nchito, imene mutu pena mcira, pena nthambi ya kanjedza, pena mlulu zidzaigwira.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 19

Onani Yesaya 19:15 nkhani