Yesaya 2:12 BL92

12 Cifukwa padzakhala tsiku la Yehova wa makamu pa zonse zonyada ndi zakudzikuza, ndi pa zonse zotukulidwa; ndipo zidzatsitsidwa;

Werengani mutu wathunthu Yesaya 2

Onani Yesaya 2:12 nkhani