11 Yehova, dzanja lanu litukulidwa, koma iwo saona; koma iwo adzaona cangu canu ca kwa anthu, nadzakhala ndi manyazi; inde moto udzamariza adani anu.
Werengani mutu wathunthu Yesaya 26
Onani Yesaya 26:11 nkhani