10 Ungayanje woipa, koma sadzaphunzira cilungamo; m'dziko la macitidwe oongoka, iye adzangocimwa, sadzaona cifumu ca Yehova.
Werengani mutu wathunthu Yesaya 26
Onani Yesaya 26:10 nkhani