Yesaya 26:14 BL92

14 Iwo afa, atha, sadzakhalanso ndi moyo; ali mizimu, sadzauka; cifukwa cace Inu munawazonda, ndi kuwaononga, mwathetsa cikumbukiro cao conse.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 26

Onani Yesaya 26:14 nkhani