19 Pakuti anthu adzakhala m'Ziyoni pa Yerusalemu; iwe sudzaliranso, Iye ndithu adzakukomera mtima pakumveka kupfuula kwako; pakumva Iye adzayankha.
Werengani mutu wathunthu Yesaya 30
Onani Yesaya 30:19 nkhani