Yesaya 30:20 BL92

20 Ndipo ngakhale Ambuye adzakupatsani inu cakudya ca nsautso, ndi madzi a cipsinjo, koma aphunzitsi ako sadzabisikanso, koma maso ako adzaona aphunzitsi ako;

Werengani mutu wathunthu Yesaya 30

Onani Yesaya 30:20 nkhani