Yesaya 33:16 BL92

16 iye adzakhala pamsanje; malo ace ocinjikiza adzakhala malinga amiyala; cakudya cace cidzapatsidwa kwa iye; madzi ace adzakhala cikhalire.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 33

Onani Yesaya 33:16 nkhani