Yesaya 35:4 BL92

4 Nenani kwa a mitima ya cinthenthe, Limbani, musaope; taonani, Mulungu wanu adza ndi kubwezera cilango, ndi mphotho ya Mulungu; Iye adzafika ndi kukupulumutsani.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 35

Onani Yesaya 35:4 nkhani