Yesaya 36:17 BL92

17 kufikira ine ndidzadza, ndi kunka nanu ku dziko lofanana ndi lanu, dziko la tirigu ndi vinyo, dziko la cakudya ndi minda yamphesa.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 36

Onani Yesaya 36:17 nkhani