Yesaya 36:18 BL92

18 Cenjerani angakukopeni inu Hezekiya, ndi kuti, Yehova adzatipulumutsa ife. Kodi milungu iri yonse ya amitundu inapulumutsa dziko lao m'manja mwa mfumu ya ku Asuri?

Werengani mutu wathunthu Yesaya 36

Onani Yesaya 36:18 nkhani