Yesaya 37:10 BL92

10 Mukati kwa Hezekiya, mfumu ya Yuda, Asakunyenge Mulungu wako, amene iwe umkhulupirira, ndi kuti, Yerusalemu sadzaperekedwa m'manja mwa mfumu ya Asuri.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 37

Onani Yesaya 37:10 nkhani