11 Taona, iwe wamva cimene mafumu a Asuri anacitira maiko onse, ndi kuwapasula konse; ndipo kodi iwe udzapulumutsidwa?
Werengani mutu wathunthu Yesaya 37
Onani Yesaya 37:11 nkhani