19 Ndipo anaponya milungu yao pamoto; pakuti iyo sinali milungu, koma nchito yopangidwa ndi manja a anthu, mtengo ndi mwala; cifukwa cace iwo anaiononga,
Werengani mutu wathunthu Yesaya 37
Onani Yesaya 37:19 nkhani