31 koma iwo amene alindira Yehova adzatenganso mphamvu; adzauluka pamwamba ndi mapiko monga ziombankhanga; adzathamanga kuma osalema; adzayenda koma osalefuka.
Werengani mutu wathunthu Yesaya 40
Onani Yesaya 40:31 nkhani