1 Khalani cete pamaso pa Ine, zisumbu inu, anthu atengenso mphamvu; ayandikire; pamenepo alankhule; tiyeni, tiyandikire pamodzi kuciweruziro.
Werengani mutu wathunthu Yesaya 41
Onani Yesaya 41:1 nkhani