15 Taona, ndidzakuyesa iwe coombera tirigu catsopano cakuthwa cokhala ndi mano; iwe udzaomba mapiri ndi kuwapera asalale, ndi kusandutsa zitunda mungu.
Werengani mutu wathunthu Yesaya 41
Onani Yesaya 41:15 nkhani