16 Iwe udzawakupa, ndi mphepo idzawauluza; ndipo kabvumvulu adzawamwaza; ndipo iwe udzasangalala mwa Yehova, udzadzikuza mwa Woyera wa Israyeli,
Werengani mutu wathunthu Yesaya 41
Onani Yesaya 41:16 nkhani