18 Ndidzagwetsa mitsinje pazitunda zoti se, ndi akasupe pakati pa zigwa; ndidzasandutsa cipululu, cikhale thamanda lamadzi, ndi mtunda wouma ukhale magwero a madzi.
Werengani mutu wathunthu Yesaya 41
Onani Yesaya 41:18 nkhani